Let words rain and reign

All writings by: Makewana's Daughters

Admin at Makewana's Daughters  •   47 articles

Let words rain and reign

Mpinimini 1


Makewana's Daughters

Mpinimini

Panangokhala, (Once upon a time) Tili tonse. Panali amai ena ake. Nde amayiwa anali a single mother. (There was a certain woman. Now this woman was a single mother). Nde basi, amai aja anayamba kudwala.
Read more

Mkazi Ng’ona 2(The crocodile wife 2)


Makewana's Daughters

9716633-vector-illustration-of-a-crocodile-on-white-background-1-1394603910

  Panangokhala                              (Once upon a time) Tili tonse Panali mtsikana wina wake     (there was a young woman) Anali pa banja.                            (who was married) Tili tonse.                               Tsopano ali ku banja kuja,       (Now, in the course of
Read more

Mpongozi (The son-in-law)


Makewana's Daughters

The-goat-and-the-rice

  Panangokhala,   (Once upon a time) Tili tonse Panali mtsikana wina wake, (There was a certain girl) Tili tonse.   Nde mtsikana uja anali wokongola kwambili (Now this girl was very beautiful) Tili tonse Anyamata
Read more

Mkazi-ng’ona (The crocodile woman)


Makewana's Daughters

9716633-vector-illustration-of-a-crocodile-on-white-background-1-1394603910

Panangokhala. (Once upon a time) Tili tonse. Panali amayi ena akenso. (There was a certain woman) Tili tonse. Anali ndi atsikana awo awiri, ana awo. (She had two daughters.) Tili tonse. Wina wamkulu, wina wamng’ono.
Read more

Dzandile ndi nkhono (Dzandile and the snail)


Makewana's Daughters

The-boy-and-the-snail

Padangokhala  (Once upon a time) Tili tonse. Padangokhala Tili tonse. Ku dziko lina lakutali ankadya nkhono. (There was a far-away country where people used to eat snails.) Tili tonse. Nde amayi ena anali ndi ana
Read more